Ekisodo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno wansembe wa ku Midiyani+ anali ndi ana aakazi 7. Iwo anafika pachitsimepo kuti atunge madzi ndi kuwathira momwera ziweto kuti ziweto za bambo awo zimwe.
16 Ndiyeno wansembe wa ku Midiyani+ anali ndi ana aakazi 7. Iwo anafika pachitsimepo kuti atunge madzi ndi kuwathira momwera ziweto kuti ziweto za bambo awo zimwe.