Ekisodo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma monga mwa masiku onse, kunafika abusa nʼkuthamangitsa atsikanawo. Zitatero Mose ananyamuka nʼkuthandiza* atsikanawo, ndipo iye anamwetsa ziweto zawo.
17 Koma monga mwa masiku onse, kunafika abusa nʼkuthamangitsa atsikanawo. Zitatero Mose ananyamuka nʼkuthandiza* atsikanawo, ndipo iye anamwetsa ziweto zawo.