Ekisodo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo anayankha kuti: “Munthu wina wa ku Iguputo+ watilanditsa kwa abusa, komanso watitungira madzi nʼkutimwetsera ziweto.”
19 Iwo anayankha kuti: “Munthu wina wa ku Iguputo+ watilanditsa kwa abusa, komanso watitungira madzi nʼkutimwetsera ziweto.”