Ekisodo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Zipora anabereka mwana wamwamuna ndipo Mose anamʼpatsa dzina lakuti Gerisomu,*+ chifukwa anati, “Ndakhala mlendo mʼdziko lachilendo.”+
22 Kenako Zipora anabereka mwana wamwamuna ndipo Mose anamʼpatsa dzina lakuti Gerisomu,*+ chifukwa anati, “Ndakhala mlendo mʼdziko lachilendo.”+