Ekisodo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Patapita nthawi yaitali mfumu ya Iguputo inamwalira.+ Koma Aisiraeli anapitirizabe kuvutika chifukwa cha ukapolo ndipo ankalira modandaula. Iwo anapitirizabe kulirira Mulungu woona+ kuti awathandize chifukwa cha ukapolowo.
23 Patapita nthawi yaitali mfumu ya Iguputo inamwalira.+ Koma Aisiraeli anapitirizabe kuvutika chifukwa cha ukapolo ndipo ankalira modandaula. Iwo anapitirizabe kulirira Mulungu woona+ kuti awathandize chifukwa cha ukapolowo.