Ekisodo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako mngelo wa Yehova anaonekera kwa iye pakati pa chitsamba chaminga+ chimene chinkayaka moto. Atachiyangʼanitsitsa, anaona kuti chitsamba chamingacho chikuyaka, koma sichikunyeka.
2 Kenako mngelo wa Yehova anaonekera kwa iye pakati pa chitsamba chaminga+ chimene chinkayaka moto. Atachiyangʼanitsitsa, anaona kuti chitsamba chamingacho chikuyaka, koma sichikunyeka.