-
Ekisodo 3:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Choncho Mose anati: “Ndipite kuti ndikaonetsetse zodabwitsa zimenezi. Ndikaone chifukwa chake chitsamba chamingachi chikuyaka koma osanyeka.”
-