Ekisodo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taona, ndamva kulira kwa Aisiraeli komanso ndaona nkhanza zimene Aiguputo akuwachitira powapondereza.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:9 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 7
9 Taona, ndamva kulira kwa Aisiraeli komanso ndaona nkhanza zimene Aiguputo akuwachitira powapondereza.+