-
Ekisodo 3:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Koma Mose anayankha Mulungu woona kuti: “Ndine ndani ine kuti ndipite kwa Farao nʼkukatulutsa Aisiraeli ku Iguputo?”
-