Ekisodo 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Mose anafunsa Mulungu woona kuti: “Nditati ndapita kwa Aisiraeli nʼkuwauza kuti, ‘Mulungu wa makolo anu wandituma kwa inu,’ iwo nʼkundifunsa kuti, ‘Dzina lake ndi ndani?’+ Ndikawayankhe kuti chiyani?” Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:13 Yandikirani, ptsa. 7-9 Nsanja ya Olonda,3/15/2013, tsa. 25
13 Koma Mose anafunsa Mulungu woona kuti: “Nditati ndapita kwa Aisiraeli nʼkuwauza kuti, ‘Mulungu wa makolo anu wandituma kwa inu,’ iwo nʼkundifunsa kuti, ‘Dzina lake ndi ndani?’+ Ndikawayankhe kuti chiyani?”