Ekisodo 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho ndidzatambasula dzanja langa nʼkulanga Iguputo ndi ntchito zanga zonse zodabwitsa zimene ndidzachite mʼdzikolo. Ndipo ndikadzachita zimenezi, adzakulolani kuti muchoke.+
20 Choncho ndidzatambasula dzanja langa nʼkulanga Iguputo ndi ntchito zanga zonse zodabwitsa zimene ndidzachite mʼdzikolo. Ndipo ndikadzachita zimenezi, adzakulolani kuti muchoke.+