Ekisodo 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako ndidzachititsa kuti Aiguputo akomere mtima anthu anga, moti pochoka simudzachoka chimanjamanja.+
21 Kenako ndidzachititsa kuti Aiguputo akomere mtima anthu anga, moti pochoka simudzachoka chimanjamanja.+