Ekisodo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Mulungu anati: “Ukachite zimenezi kuti akakhulupirire kuti Yehova Mulungu wa makolo awo, Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo,+ anaonekera kwa iwe.”+
5 Kenako Mulungu anati: “Ukachite zimenezi kuti akakhulupirire kuti Yehova Mulungu wa makolo awo, Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo,+ anaonekera kwa iwe.”+