Ekisodo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova anamuuzanso kuti: “Lowetsa dzanja lako mʼmalaya, pachifuwa.” Choncho Mose analowetsa dzanja lake mʼmalaya. Koma atalitulutsa, anaona kuti dzanja lakelo lachita khate ndipo likuoneka loyera kwambiri.+
6 Yehova anamuuzanso kuti: “Lowetsa dzanja lako mʼmalaya, pachifuwa.” Choncho Mose analowetsa dzanja lake mʼmalaya. Koma atalitulutsa, anaona kuti dzanja lakelo lachita khate ndipo likuoneka loyera kwambiri.+