-
Ekisodo 4:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndiyeno Mulungu anati: “Lowetsanso dzanja lako mʼmalayamo.” Choncho analowetsanso dzanja lake mʼmalaya. Atalitulutsa anaona kuti lakhalanso bwino ngati poyamba.
-