Ekisodo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komabe ngati sakakhulupirira zizindikiro ziwirizi nʼkumvera mawu ako, ukatenge madzi amumtsinje wa Nailo nʼkuwathira panthaka youma. Ndipo madzi amene ukatenge mumtsinje wa Nailowo adzasanduka magazi panthakapo.”+
9 Komabe ngati sakakhulupirira zizindikiro ziwirizi nʼkumvera mawu ako, ukatenge madzi amumtsinje wa Nailo nʼkuwathira panthaka youma. Ndipo madzi amene ukatenge mumtsinje wa Nailowo adzasanduka magazi panthakapo.”+