Ekisodo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Mose anauza Yehova kuti: “Pepani Yehova, ine kulankhula kumandivuta kuyambira kalekale. Komanso panopa pamene mukulankhula ndi ine mtumiki wanu, ndikulankhula movutikira* chifukwa ndine wa lilime lolemera.”+
10 Ndiyeno Mose anauza Yehova kuti: “Pepani Yehova, ine kulankhula kumandivuta kuyambira kalekale. Komanso panopa pamene mukulankhula ndi ine mtumiki wanu, ndikulankhula movutikira* chifukwa ndine wa lilime lolemera.”+