Ekisodo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho ukalankhule naye ndi kumuuza zoti akanene.+ Ineyo ndidzakhala ndi iwe pamodzi ndi iye mukamakalankhula+ ndipo ndidzakuuzani zochita.
15 Choncho ukalankhule naye ndi kumuuza zoti akanene.+ Ineyo ndidzakhala ndi iwe pamodzi ndi iye mukamakalankhula+ ndipo ndidzakuuzani zochita.