Ekisodo 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Mose anapita kwa Yetero apongozi ake+ nʼkuwauza kuti: “Ndikufuna kupita kwa abale anga ku Iguputo kuti ndikaone ngati adakali moyo.” Choncho, Yetero anayankha Mose kuti: “Pita mu mtendere.”
18 Choncho Mose anapita kwa Yetero apongozi ake+ nʼkuwauza kuti: “Ndikufuna kupita kwa abale anga ku Iguputo kuti ndikaone ngati adakali moyo.” Choncho, Yetero anayankha Mose kuti: “Pita mu mtendere.”