-
Ekisodo 4:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Kenako Mose anatenga mkazi wake ndi ana ake nʼkuwakweza pabulu, ndipo anayamba ulendo wobwerera ku Iguputo. Komanso Mose anatenga ndodo ya Mulungu woona mʼdzanja lake.
-