Ekisodo 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anauzanso Mose kuti: “Ukakafika ku Iguputo ukaonetsetse kuti wachita pamaso pa Farao, zodabwitsa zonse zimene ndakupatsa mphamvu kuti ukachite.+ Koma ine ndidzamulola kuti aumitse mtima wake,+ moti sadzalola anthu anga kuchoka.+
21 Yehova anauzanso Mose kuti: “Ukakafika ku Iguputo ukaonetsetse kuti wachita pamaso pa Farao, zodabwitsa zonse zimene ndakupatsa mphamvu kuti ukachite.+ Koma ine ndidzamulola kuti aumitse mtima wake,+ moti sadzalola anthu anga kuchoka.+