Ekisodo 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Yehova anauza Aroni kuti: “Pita kuchipululu kukachingamira Mose.”+ Choncho Aroni ananyamuka ndipo anakumana ndi Mose paphiri la Mulungu woona,+ ndipo anamulonjera nʼkumukisa.*
27 Kenako Yehova anauza Aroni kuti: “Pita kuchipululu kukachingamira Mose.”+ Choncho Aroni ananyamuka ndipo anakumana ndi Mose paphiri la Mulungu woona,+ ndipo anamulonjera nʼkumukisa.*