Ekisodo 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Atakumana, Mose anauza Aroni mawu onse a Yehova, yemwe anamutuma.+ Anamuuzanso zizindikiro zonse zimene anamulamula kuti achite.+
28 Atakumana, Mose anauza Aroni mawu onse a Yehova, yemwe anamutuma.+ Anamuuzanso zizindikiro zonse zimene anamulamula kuti achite.+