Ekisodo 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Zitatero anthuwo anakhulupirira+ Mose. Atamva kuti Yehova akufuna kuthandiza Aisiraeli+ komanso kuti waona mavuto amene akukumana nawo,+ anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi.
31 Zitatero anthuwo anakhulupirira+ Mose. Atamva kuti Yehova akufuna kuthandiza Aisiraeli+ komanso kuti waona mavuto amene akukumana nawo,+ anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi.