-
Ekisodo 5:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako Mose ndi Aroni anapita kwa Farao nʼkumuuza kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Lola anthu anga apite mʼchipululu kuti akachite chikondwerero.’”
-