Ekisodo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Farao anati: “Yehova ndi ndani+ kuti ndimvere mawu ake nʼkulola Aisiraeli kuti apite?+ Ine sindikumudziwa Yehova ngakhale pangʼono ndipo sindilola kuti Aisiraeli apite.”+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:2 Nsanja ya Olonda,7/15/1993, ptsa. 3-52/1/1988, tsa. 24
2 Koma Farao anati: “Yehova ndi ndani+ kuti ndimvere mawu ake nʼkulola Aisiraeli kuti apite?+ Ine sindikumudziwa Yehova ngakhale pangʼono ndipo sindilola kuti Aisiraeli apite.”+