Ekisodo 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komabe iwo anati: “Mulungu wa Aheberi walankhula nafe. Ndiye mutilole chonde, tipite ulendo wamasiku atatu mʼchipululu, kuti tikapereke nsembe kwa Yehova Mulungu wathu.+ Ngati sititero, adzatipha ndi matenda kapena lupanga.”
3 Komabe iwo anati: “Mulungu wa Aheberi walankhula nafe. Ndiye mutilole chonde, tipite ulendo wamasiku atatu mʼchipululu, kuti tikapereke nsembe kwa Yehova Mulungu wathu.+ Ngati sititero, adzatipha ndi matenda kapena lupanga.”