Ekisodo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Anthu amenewa musawapatsenso udzu woumbira njerwa.+ Muwasiye azikafuna okha udzu umenewo.