Ekisodo 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako oyangʼanira ntchito a Farao anamenya+ akapitawo a Aisiraeli amene iwo anawaika nʼkuwafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani dzulo ndi lero simunamalize kuumba njerwa zimene munauzidwa ngati mmene munkachitira poyamba?”
14 Kenako oyangʼanira ntchito a Farao anamenya+ akapitawo a Aisiraeli amene iwo anawaika nʼkuwafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani dzulo ndi lero simunamalize kuumba njerwa zimene munauzidwa ngati mmene munkachitira poyamba?”