Ekisodo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinkaonekera kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse kwa iwo.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:3 Nsanja ya Olonda,3/15/2004, tsa. 2511/15/1989, tsa. 4
3 Ndinkaonekera kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse kwa iwo.+