Ekisodo 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ine ndamva kubuula kwa Aisiraeli, amene Aiguputo akuwagwiritsa ntchito yaukapolo, ndipo ndikukumbukira pangano langa.+
5 Tsopano ine ndamva kubuula kwa Aisiraeli, amene Aiguputo akuwagwiritsa ntchito yaukapolo, ndipo ndikukumbukira pangano langa.+