Ekisodo 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Mose anayankha Yehova kuti: “Komatu Aisiraeli sanandimvere,+ ndiye Farao akandimvera bwanji? Pajatu ndimalankhula movutikira.”*+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:12 Nsanja ya Olonda,12/15/2015, tsa. 15
12 Koma Mose anayankha Yehova kuti: “Komatu Aisiraeli sanandimvere,+ ndiye Farao akandimvera bwanji? Pajatu ndimalankhula movutikira.”*+