Ekisodo 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atsogoleri a mafuko a Aisiraeli ndi awa: Ana aamuna a Rubeni, yemwe anali mwana woyamba kubadwa wa Isiraeli,+ anali Hanoki, Palu, Hezironi ndi Karami.+ Amenewa ndi mabanja a fuko la Rubeni.
14 Atsogoleri a mafuko a Aisiraeli ndi awa: Ana aamuna a Rubeni, yemwe anali mwana woyamba kubadwa wa Isiraeli,+ anali Hanoki, Palu, Hezironi ndi Karami.+ Amenewa ndi mabanja a fuko la Rubeni.