Ekisodo 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana aamuna a Simiyoni anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Shauli, mwana amene anabereka ndi mkazi wa Chikanani.+ Amenewa ndi mabanja a fuko la Simiyoni.
15 Ana aamuna a Simiyoni anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Shauli, mwana amene anabereka ndi mkazi wa Chikanani.+ Amenewa ndi mabanja a fuko la Simiyoni.