Ekisodo 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Umenewu ndi mzere wobadwira wa Aroni ndi Mose, amene Yehova anawauza kuti: “Tulutsani Aisiraeli mʼdziko la Iguputo mʼmagulumagulu.”*+
26 Umenewu ndi mzere wobadwira wa Aroni ndi Mose, amene Yehova anawauza kuti: “Tulutsani Aisiraeli mʼdziko la Iguputo mʼmagulumagulu.”*+