-
Ekisodo 7:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Iwe uzimuuza zonse zimene ndizikulamula, koma Aroni mchimwene wako ndi amene azikalankhula ndi Farao, ndipo adzaloladi Aisiraeli kuti achoke mʼdziko lake.
-