Ekisodo 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe Farao sadzakumverani, choncho ndidzaonetsa mphamvu ya dzanja langa pa Iguputo ndi kutulutsa anthu anga Aisiraeli omwe ndi ambiri. Ndidzawatulutsa mʼdziko la Iguputo ndi ziweruzo zamphamvu.+
4 Komabe Farao sadzakumverani, choncho ndidzaonetsa mphamvu ya dzanja langa pa Iguputo ndi kutulutsa anthu anga Aisiraeli omwe ndi ambiri. Ndidzawatulutsa mʼdziko la Iguputo ndi ziweruzo zamphamvu.+