Ekisodo 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova+ ndikadzatambasula dzanja langa ndi kulanga Iguputo, nʼkutulutsa Aisiraeli mʼdzikolo.”
5 Pamenepo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova+ ndikadzatambasula dzanja langa ndi kulanga Iguputo, nʼkutulutsa Aisiraeli mʼdzikolo.”