Ekisodo 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komabe, Farao anaitana amuna anzeru ndi amatsenga ndipo ansembe ochita zamatsenga a ku Iguputo+ nawonso anachita zomwezo mwa matsenga awo.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:11 Nsanja ya Olonda,1/15/1996, tsa. 24
11 Komabe, Farao anaitana amuna anzeru ndi amatsenga ndipo ansembe ochita zamatsenga a ku Iguputo+ nawonso anachita zomwezo mwa matsenga awo.+