Ekisodo 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ngakhale zinali choncho, Farao anaumitsabe mtima wake+ ndipo sanawamvere, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena.
13 Ngakhale zinali choncho, Farao anaumitsabe mtima wake+ ndipo sanawamvere, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena.