Ekisodo 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiye ukamuuze kuti, ‘Yehova Mulungu wa Aheberi wandituma kwa iwe+ ndi uthenga wakuti: “Lola anthu anga kuchoka kuti akanditumikire mʼchipululu,” koma mpaka pano sukundimvera.
16 Ndiye ukamuuze kuti, ‘Yehova Mulungu wa Aheberi wandituma kwa iwe+ ndi uthenga wakuti: “Lola anthu anga kuchoka kuti akanditumikire mʼchipululu,” koma mpaka pano sukundimvera.