Ekisodo 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zitatero nsomba zamumtsinje wa Nailo zinafa+ ndipo mtsinjewo unayamba kununkha. Aiguputo sanathenso kumwa madzi amumtsinje wa Nailo.+ Mʼdziko lonse la Iguputo munali magazi okhaokha.
21 Zitatero nsomba zamumtsinje wa Nailo zinafa+ ndipo mtsinjewo unayamba kununkha. Aiguputo sanathenso kumwa madzi amumtsinje wa Nailo.+ Mʼdziko lonse la Iguputo munali magazi okhaokha.