Ekisodo 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma ansembe ochita zamatsenga a ku Iguputo anachitanso zomwezo mwa matsenga awo,+ moti Farao anapitiriza kuumitsa mtima wake, ndipo sanamvere Mose ndi Aroni, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:22 Nsanja ya Olonda,3/15/2004, tsa. 25
22 Koma ansembe ochita zamatsenga a ku Iguputo anachitanso zomwezo mwa matsenga awo,+ moti Farao anapitiriza kuumitsa mtima wake, ndipo sanamvere Mose ndi Aroni, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena.+