-
Ekisodo 8:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Uza Aroni kuti, ‘Tambasula dzanja lako nʼkulozetsa ndodo yako kumitsinje, kungalande zochokera kumtsinje wa Nailo ndi kuzithaphwi, kuti achule atuluke mmenemo nʼkubwera pamtunda mʼdziko lonse la Iguputo.’”
-