Ekisodo 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Farao ataona kuti mliri wa achulewo watha, anaumitsa mtima wake,+ ndipo sanamvere Mose ndi Aroni, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena.
15 Farao ataona kuti mliri wa achulewo watha, anaumitsa mtima wake,+ ndipo sanamvere Mose ndi Aroni, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena.