Ekisodo 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ansembe ochita zamatsenga anayesanso kuti apange tizilombo toyamwa magazi pogwiritsa ntchito matsenga awo,+ koma analephera. Ndipo tizilomboto tinkasowetsa mtendere anthu ndi nyama zomwe.
18 Ansembe ochita zamatsenga anayesanso kuti apange tizilombo toyamwa magazi pogwiritsa ntchito matsenga awo,+ koma analephera. Ndipo tizilomboto tinkasowetsa mtendere anthu ndi nyama zomwe.