Ekisodo 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ataona zimenezi ansembe ochita zamatsenga aja anauza Farao kuti: “Chimenechi ndi chala cha Mulungu!”+ Koma Farao anapitiriza kuumitsa mtima wake ndipo sanawamvere, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:19 Nsanja ya Olonda,6/15/1987, tsa. 5
19 Ataona zimenezi ansembe ochita zamatsenga aja anauza Farao kuti: “Chimenechi ndi chala cha Mulungu!”+ Koma Farao anapitiriza kuumitsa mtima wake ndipo sanawamvere, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena.