Ekisodo 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa tsiku limenelo ndidzapatula dera la Goseni kumene kuli anthu anga. Kumeneko sikudzakhala ntchentche zoluma.+ Ndidzachita zimenezi kuti udziwe kuti ine Yehova, ndili mʼdziko lino.+
22 Pa tsiku limenelo ndidzapatula dera la Goseni kumene kuli anthu anga. Kumeneko sikudzakhala ntchentche zoluma.+ Ndidzachita zimenezi kuti udziwe kuti ine Yehova, ndili mʼdziko lino.+