Ekisodo 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova anachitadi zimenezi tsiku lotsatira, moti ziweto zamitundu yonse za Aiguputo zinayamba kufa,+ koma palibe chiweto ngakhale chimodzi cha Aisiraeli chimene chinafa.
6 Yehova anachitadi zimenezi tsiku lotsatira, moti ziweto zamitundu yonse za Aiguputo zinayamba kufa,+ koma palibe chiweto ngakhale chimodzi cha Aisiraeli chimene chinafa.