-
Ekisodo 9:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Choncho iwo anatenga phulusa la mu uvuni nʼkuima pamaso pa Farao. Kenako Mose analiponya mʼmwamba ndipo linayambitsa zithupsa zimene zinkaphulika pa anthu ndi nyama.
-